Zamkatimu
Zamkatimu
April 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MLUNGU WA:
May 26, 2008–June 1, 2008
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 48, 20
June 2-8, 2008
Mulungu Azikutsogolerani M’zinthu Zonse
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 131, 225
June 9-15, 2008
Achinyamata, Kumbukirani Mlengi Wanu Wamkulu
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 157, 183
June 16-22, 2008
Kukwatira Ndiponso Kukhala ndi Ana M’nthawi Yamapeto Ino
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 24, 164
June 23-29, 2008
Kodi Chofunika Ndi Chiyani Kuti Tikhale ndi Moyo Waphindu?
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 214, 67
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhani ziwirizi zikutithandiza kuzindikira “zinthu zopanda pake,” zinthu zomwe zingatilepheretse kutumikira Yehova. Zikufotokoza misampha imene ingathe kutikola mosavuta, ndipo zikupereka zifukwa zambiri zimene tiyenera kuyang’anira kwa Yehova kuti azititsogolera m’zinthu zonse.
Nkhani Zophunzira 3, 4 MASAMBA 12-20
Yoyamba ikuuza achinyamata kuti Baibulo lingawathandize kusankha zochita zimene zingasinthe moyo wawo. Yachiwiri ikuwapatsa malangizo abwino a m’Malemba a zimene ayenera kuganizira akafuna kukwatira kapena kukhala ndi ana.
Nkhani Zophunzira 5 MASAMBA 21-5
Nkhani yomalizayi ikufotokoza mfundo zochititsa chidwi za m’buku la Mlaliki. Ikutchula zinthu zofunikadi pamoyo, ndipo ikuzisiyanitsa ndi zinthu zimene dzikoli limalimbikitsa.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Tisawaiwale Ngakhale Amakhala Kwaokha
TSAMBA 25
TSAMBA 29
Mawu a Yehova Ndi Amoyo Mfundo Zazikulu za M’buku la Yohane
TSAMBA 30