Zamkatimu
Zamkatimu
August 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
September 29, 2008–October 5, 2008
Yehova Sataya Anthu Ake Okhulupirika
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 114, 223
October 6-12, 2008
Khalani Okhulupirika ndi Mtima Wonse
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 38, 8
October 13-19, 2008
Lemekezani Yehova mwa Kusonyeza Ulemu
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 48, 136
October 20-26, 2008
Yehova Amasamalira Mwachikondi Atumiki Ake Okalamba
TSAMBA 17
NYIMBO ZOIMBA: 58, 216
October 27, 2008–November 2, 2008
Kodi Mumalankhula Bwino “Chinenero Choyera”?
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 78, 169
Cholinga Cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Zimene zinachitika panthawi imene mafuko 12 a Isiraeli anagawidwa kukhala ufumu wa kumpoto ndi wa kumwera, zikutiphunzitsa kuti Yehova sataya anthu ake okhulupirika. Nkhanizi zikugogomezera kuti tifunika kukhala okhulupirika ndi mtima wonse panopa kuti tipewe mtima wokonda chuma kapena wodzikuza.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 12-16
Nkhaniyi ikutiphunzitsa zimene tiyenera kuchita pozindikira ukulu wa Mulungu. Ikufotokoza zimene tikuphunzira kwa Yesu pankhani yosonyeza anthu ulemu ndipo ikutiphunzitsanso mmene tingasonyezere ulemu.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 17-21
Phunzirani kuwaona Akhristu okalamba mmene Yehova amawaonera. Muonanso mmene Baibulo limatithandizira kuti tizilemekeza zimene akudziwa, mmene akumvera, ndiponso kuwathandiza kukhalabe achangu pazochita zachikhristu.
Nkhani Yophunzira 5 MASAMBA 21-25
Kudzera mwa mneneri wake Zefaniya, Yehova anati: “Ndidzapatsa mitundu ya anthu mlomo woyera [“chinenero choyera,” NW].” (Zef. 3:9) Muphunzira kuti “chinenero choyera” n’chiyani. Onani zimene mungachite kuti muzilankhula bwino chinenerochi. Onaninso mmene mungagwiritsire ntchito chinenero chapaderachi potamanda Yehova.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
TSAMBA 26
TSAMBA 29
TSAMBA 30