Zamkatimu
Zamkatimu
September 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
November 3-9, 2008
Yehova ‘Anapulumutsa’ Anthu Ake M’nthawi za m’Baibulo
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 74, 44
November 10-16, 2008
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 153, 3
November 17-23, 2008
Khalanibe ndi “Chingwe cha Nkhosi Zitatu” M’banja Lanu
TSAMBA 16
NYIMBO ZOIMBA: 117, 173
November 24-30, 2008
TSAMBA 20
NYIMBO ZOIMBA: 10, 191
Cholinga Cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhanizi zachokera pa Salmo 70. Pamenepo timapezapo mawu akuti Yehova ndi “mpulumutsi.” Nkhanizi zikufotokoza mmene Yehova anapulumutsira atumiki ake m’nthawi za m’Baibulo ndiponso mmene amatipulumutsira masiku ano.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 16-20
Masiku ano n’zovuta kuti anthu okwatirana akhale ogwirizana, ngakhale anthuwo atakhala atumiki a Yehova. M’nkhaniyi muli mfundo zothandiza zimene Akhristu angatsatire kuti Yehova akhale m’banja lawo, komanso zimene angachite pakakhala mavuto.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 20-24
Timafunika kusankha pakati pa zinthu ziwiri izi: Kutsogoleredwa ndi mzimu woyera wa Mulungu kapena ndi mzimu wa dzikoli. Nkhaniyi ikufotokoza zimene tingachite kuti mzimu wa Mulungu uzititsogolera komanso mmene tingapewere mzimu wa dziko. Ndipo itithandizanso kusankha zinthu zimene zingatipangitse kukhala osangalala.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
Wonjezerani Chidwi Chofuna Kudziwa Zinthu Molondola
TSAMBA 12
TSAMBA 25
Tsanzirani Yesu—Lambirani Mulungu Moyenera
TSAMBA 26
Mawu a Yehova Ndi Amoyo—Mfundo Zazikulu za M’makalata Opita kwa Atesalonika ndi Timoteyo
TSAMBA 29
TSAMBA 32