Zamkatimu
Zamkatimu
October 15, 2008
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
December 1-7, 2008
“Maso Onyezimira” a Yehova Amasanthula Anthu Onse
TSAMBA 3
NYIMBO ZOIMBA: 160, 34
December 8-14, 2008
Yehova Amatiyang’ana ndi Zolinga Zabwino
TSAMBA 7
NYIMBO ZOIMBA: 81, 80
December 15-21, 2008
Mmene Yehova Akuyankhira Pemphero Lochokera Pansi Pamtima
TSAMBA 12
NYIMBO ZOIMBA: 74, 90
December 22-28, 2008
Kodi Mumakhala Patsogolo Posonyeza Ulemu?
TSAMBA 21
NYIMBO ZOIMBA: 216, 155
December 29, 2008–January 4, 2009
Kodi Mungalolere Kudzimana Chiyani Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha?
TSAMBA 25
NYIMBO ZOIMBA: 177, 212
Cholinga Cha Nkhani Zophunzira
Nkhani Zophunzira 1, 2 MASAMBA 3-11
Nkhani ziwiri zimenezi zikutitsimikizira kuti Yehova amadziwa zonse zimene zimatichitikira. Amaona kupirira kwathu komanso amadziwa mavuto athu. Amaona kulimbikira kwathu konse komanso zimene zimachitikira atumiki ake. Kudziwa zimenezi n’kolimbikitsa.
Nkhani Yophunzira 3 MASAMBA 12-16
Ambirife timadziwa mawu a pa Salmo 83:18. Nanga bwanji za salmo lonselo? Nkhani imeneyi ikusonyeza kuti Salmo 83 lingalimbikitse kwambiri Akhristu masiku ano.
Nkhani Yophunzira 4 MASAMBA 21-25
Paulo ananena kuti: “Posonyezana ulemu wina ndi mnzake, khalani patsogolo.” Kodi kusonyeza ena ulemu kumatanthauza chiyani? Kodi ndani ayenera kusonyeza ulemu, nanga ndani ayenera kulemekezedwa? Kodi tili ndi zitsanzo zotani za m’Baibulo? Nkhani imeneyi ili ndi mfundo zothandiza.
Nkhani Yophunzira 5 MASAMBA 25-29
Tsiku lina Yesu anafunsa kuti: “Kodi munthu angapereke chiyani chosinthanitsa ndi moyo wake?” Kodi mungayankhe bwanji funso limeneli? Kodi zochita zanu zimasonyeza kuti mumakonda kwambiri moyo wanu? Nkhaniyi ikuthandizani kuganizira mofatsa funso la Yesu lofunika kwambiri limeneli.
M’MAGAZINI INO MULINSO:
“Ilitu Ndi Dzina Loyera Ndiponso Lalikulu la Mulungu”
TSAMBA 16
TSAMBA 17
Mawu a Yehova Ndi Amoyo—Mfundo Zazikulu za M’makalata Opita kwa Tito, Filemoni ndi Aheberi
TSAMBA 30