Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2008
Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2008
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
Baibulo Limasintha Anthu, 8/1
Kodi Mungadziwe Bwanji Baibulo Lomasuliridwa Bwino? 5/1
Kodi Ndani Angadziwe Zam’tsogolo? 10/1
Kodi Nkhani za M’mabuku a Uthenga Wabwino N’zenizeni? 10/1
Mfundo Zazikulu za M’buku la Luka, 3/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Machitidwe, 5/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Maliko, 2/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Mateyo, 1/15
Mfundo Zazikulu za M’buku la Yohane, 4/15
Mfundo Zazikulu za M’kalata ya Aroma, 6/15
Mfundo Zazikulu za M’makalata a ku Korinto, 7/15
Mfundo Zazikulu za M’makalata a Yakobe ndi Petulo, 11/15
Mfundo Zazikulu za M’makalata a Yohane ndi Yuda, 12/15
Mfundo Zazikulu za mu Agalatiya, Aefeso, Afilipi, ndi Akolose, 8/15
Mfundo Zazikulu za mu Atesalonika ndi Timoteyo, 9/15
Mfundo Zazikulu za mu Tito, Filemoni ndi Aheberi, 10/15
Mmene Mawu Anakhalira Malemba Opatulika, 9/1
MpukutuWotchedwa “Nyimbo ya Panyanja,” 11/15
Zolemba Zakale Zimatsimikizira Kuti Baibulo N’lolondola, 12/15
MBIRI YA MOYO WANGA
“Anditsogolera M’mabande a Chilungamo” (O. Campbell), 3/1
Chikhulupiriro Chinandithandiza Kupirira Mavuto (S. Castillo), 10/1
Kufufuza Zolakwa Kunandidziwitsa Choonadi (R. S. Marshall), 12/1
Mulungu Wandichitira Chifundo Kwambiri (B. Močnik), 7/1
Ndasangalala Pochita Chifuniro cha Mulungu (B. Yaremchuk), 6/1
Ndaona Mboni Zikuwonjezereka ku Korea (M. Hamilton), 12/15
Ndinamasuka ku Mikwingwirima ya Paubwana (E. Morcillo), 1/1
Sitinachite Mantha, Yehova Anali Nafe (E. Petridou), 7/15
“Usakaleke Kulalikira ku Nyumba ndi Nyumba” (J. Neufeld), 9/1
“Yehova Ndiye Mphamvu Yanga” (J. Coville), 10/15
MBONI ZA YEHOVA
Baibulo Limasintha Anthu, 8/1
Chionetsero Chokhala ndi Cholinga (South Africa), 11/1
“Kamtsikana Kachiisiraeli” Kamakono, 6/1
Kodi Amakhulupirira Kuti Ndiwo Okha Adzapulumuke? 11/1
Kodi Amathetsa Maukwati a Anthu? 11/1
Kodi Zimakhulupirira Chipangano Chakale? 12/1
Kufalitsa Uthenga Wabwino M’mapiri a Andes, 3/15
Kulalikira Pamsika, 9/15
Kumanga Nyumba Zotamandiramo Yehova (Nyumba za Ufumu m’Mexico, Belize), 2/1
Kufotokoza za Chikhulupiriro Chanu (mtsikana wa ku sukulu), 6/15
Kutumikira Mulungu ndi “Mtima Umodzi ndi Maganizo Amodzi” (zopereka), 11/15
Kwa Owerenga (zatsopano mu Nsanja ya Olonda), 1/1
Nsanja ya Olonda Yophunzira, 1/15
Misonkhano Yakuti “Mzimu wa Mulungu Umatitsogolera”, 3/1
Mmene Bungwe Lolamulira Limayendetsera Ntchito Zake, 5/15
Mtundu wa Amaya Wapeza Ufulu Weniweni, 12/1
N’chifukwa Chiyani Sizigwiritsa Ntchito Mtanda Polambira? 3/1
N’chifukwa Chiyani Sizimenya Nawo Nkhondo? 7/1
“Ndikawerenga Bukuli Pootha Moto Usiku Uno,” 6/1
Ndinazindikira Kuti Moyo Ndi WamtengoWapatali, 9/1
Nzeru Yothandiza (kupita ku msonkhano wachigawo), 6/15
Omaliza Maphunziro a Gileadi, 2/15, 8/15
Ozunzidwa Apatsidwa Ufulu (Republic of Georgia), 3/1
“Pa Mtsinje wa Coco, Mukakhotere Kumanja,” 9/1
Pangano Lofunika Kwambiri, 3/15
“Sindinaonepo Chikondi Ngati Ichi” (Dominican Republic), 3/1
Tsiku Limene Ndinasiya Karate, 12/1
Tsoka Lalikulu ku Solomon Islands, 5/1
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Abale Ake a Yosefe Anachita Nsanje—Umachita Nsanje? 10/1
Akhristu Akamapetedwa Ngati Tirigu, 1/15
Ankafuna Kuthandiza Ena, 6/1
Azimayi—Khalani ndi Moyo Wosangalala, 2/1
Ganizirani Mapeto Ake, 9/1
Khalanibe Okhulupirika Muukwati Wanu, 11/1
“Khalani Otsanzira Mulungu,” 10/1
Khalani ‘Oyera Poopa Mulungu,’ 5/15
Kodi Mukumanga Pamchenga Kapena Pathanthwe? 11/1
Kodi Mumachita Chidwi ndi Zinthu? 6/1
Kodi Mumafuna Mutakhala Munthu Wotani? 11/15
Kodi Mungatani Kuti Mukhale Bambo Wabwino? 10/1
Kodi Zimene Mukufuna Kuchita Zikugwirizana ndi Cholinga cha Mulungu? 7/1
Kulankhulana ndi Achinyamata, 8/1
Kulera Bwino Ana M’dziko Lolekererali, 4/1
Kulimbikitsa Amene Ali ndi Matenda Oti Afa Nawo, 5/1
Kuthandiza Mwana Wanu Panthawi Yachisoni, 7/1
Kuthetsa Mavuto, 5/1
Kuthetsa Mikangano (m’banja), 2/1
Limbikitsani Banja Lanu ndi “Mawu Okondweretsa,” 1/1
Mmene Tiyenera Kukhalira ndi Ena, 8/1
Moyo Wawo Unakhala Waphindu, 1/15
Mungamasangalale Ngakhale Pali Zokhumudwitsa, 3/1
Musadzipanikize, Ndipo Mudzakhala Achimwemwe, 7/15
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusonyeza Kuti Timayamikira? 8/1
N’chifukwa Chiyani Ukhondo Uli Wofunika? 12/1
Samueli Anapitirizabe Kuchita Zabwino, 8/1
Tingakhale Amphamvu Ngakhale Tili ndi Zofooka, 6/15
Tisawaiwale Ngakhale Amakhala Kwaokha (malo osungirako okalamba), 4/15
Titengerepo Phunziro Pazolakwa za Aisiraeli, 2/15
“Titsatire Zinthu Zodzetsa Mtendere,” 11/15
Tsanzirani Yesu—Lambirani Mulungu Moyenera, 9/15
Wonjezerani Kudziwa Zinthu Molondola, 9/15
NKHANI ZOPHUNZIRA
Achinyamata, Kumbukirani Mlengi Wanu Wamkulu, 4/15
Amene Ali ndi “Maganizo Oyenerera” Akulabadira, 1/15
Athandizeni Kubwerera Mwamsanga! 11/15
Chipulumutso mwa Ufumu wa Mulungu Chayandikira! 5/15
Chitirani Umboni Bwino Lomwe, 12/15
Gonjerani Ulamuliro wa Yehova, 6/15
Ikani Yehova Patsogolo Panu Nthawi Zonse, 2/15
Kanani Zinthu “Zopanda Pake,” 4/15
Khalanibe ndi “Chingwe cha Nkhosi Zitatu” M’banja, 9/15
Khalani Okhulupirika ndi Mtima Wonse, 8/15
Khalani Ololera Koma Mosapitirira Malire, 3/15
Kodi Chofunika Ndi Chiyani Kuti Tikhale ndi Moyo Waphindu? 4/15
Kodi Kukhalapo kwa Khristu Kumatanthauza Chiyani kwa Inu? 2/15
Kodi Mudzasungabe Umphumphu? 12/15
Kodi Mumakhala Patsogolo Posonyeza Ulemu? 10/15
Kodi Mumalankhula Bwino “Chinenero Choyera”? 8/15
Kodi Mumaona Anthu Mmene Yehova Amawaonera? 3/15
Kodi Mungalolere Kudzimana Chiyani Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha? 10/15
Kodi Tingatani ndi Mavuto Amene Timakumana Nawo Muutumiki wa ku Nyumba ndi Nyumba? 7/15
Kodi Tizikhala Bwanji ndi Anzathu? 5/15
“Kodi Wanzeru ndi Womvetsa Zinthu Ndani Pakati pa Inu?” 3/15
Kukwatira Ndiponso Kukhala ndi Ana M’nthawi Yamapeto Ino, 4/15
Lemekezani Yehova mwa Kusonyeza Ulemu, 8/15
Makhalidwe Amene Tiyenera Kutsatira, 6/15
“Maso Onyezimira” a Yehova Amasanthula Anthu Onse, 10/15
Mmene Yehova Akuyankhira Pemphero Lochokera Pansi Pamtima, 10/15
Mulungu Azikutsogolerani M’zinthu Zonse, 4/15
‘Mulungu Ndi Amene Amakulitsa’! 7/15
Musasiye ‘Chikondi Chimene Munali Nacho Poyamba,’ 6/15
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kusunga Umphumphu? 12/15
N’chifukwa Chiyani Utumiki wa ku Nyumba ndi Nyumba Uli Wofunika Kwambiri Masiku Ano? 7/15
Onetsetsani Kuti Mukusamala Utumiki Umene Munaulandira mwa Ambuye, 1/15
Oyenerera Kulandira Ufumu, 1/15
Oyenerera Kutsogoleredwa ku Akasupe a Madzi a Moyo, 1/15
Pewani “Mzimu wa Dziko,” 9/15
Pitani Patsogolo Mwauzimu Potsanzira Paulo, 5/15
Pitirizani Kuchita Zabwino, 5/15
Samalirani Thanzi Lanu M’njira Yogwirizana ndi Malemba, 11/15
Sangalalani mu Ukwati Wanu, 3/15
Sankhani Kutumikira Yehova Mudakali Achinyamata, 5/15
Simudziwa Zimene Zidzalola, 7/15
Thandizani Osochera Kubwerera M’gulu la Nkhosa, 11/15
Tsanzirani Mmishonale Woposa Amishonale Onse, 2/15
“Tsutsani Mdyerekezi” Monga Anachitira Yesu, 11/15
Udindo Wapadera wa Yesu Pokwaniritsa Cholinga cha Mulungu, 12/15
Yang’anirani ‘Luso Lanu la Kuphunzitsa,’ 1/15
Yehova Amamva Kulira Kwathu Ndipo Amatithandiza, 3/15
Yehova Amasamalira Mwachikondi Atumiki Ake Okalamba, 8/15
Yehova Amatiyang’ana ndi Zolinga Zabwino, 10/15
Yehova ‘Anapulumutsa’ Anthu Ake M’nthawi za m’Baibulo, 9/15
Yehova Ndi “Mpulumutsi” Wathu, 9/15
Yehova Sataya Anthu Ake Okhulupirika, 8/15
Yendani M’njira za Yehova, 2/15
Yesu Khristu—Mmishonale Woposa Amishonale Onse, 2/15
Zinthu Zimene Tiyenera Kuthawa, 6/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Akhristu M’nthawi ya Ulamuliro wa Agiriki, 12/1
Analingalira Mawuwo Mumtima Mwake’ (Mariya), 10/1
Anali Watcheru Ndiponso Anadikira (Eliya), 4/1
Anthu Ambiri Amakhulupirira za Helo, 11/1
Aramagedo, 4/1
Aramagedo Idzamenyedwera Kuti? 4/1
Chigumula cha Nowa, 6/1
“Chilamulo Chakhala Namkungwi,” 3/1
Chiwembu Chibwerera Eni Ake (Danieli), 11/1
Cholinga cha Moyo, 2/1
‘Kalata ya Chilekanitso,’ 9/1
Kodi Chimachitika N’chiyani Munthu Akamwalira? 11/1
Kodi Dziko Lapansi Lidzawonongedwa? 4/1
Kodi Dziko Lapansili Likhalapobe Mpaka Kalekale? 8/1
Kodi Ayuda Onse Adzatembenuka N’kukhala Akhristu? (Aro 11:26), 6/15
Kodi Zinatheka Bwanji Kuti Adamu Achimwe? 10/1
Kodi Matenda a Dzikoli Ndi Ochiritsika? 9/1
Kodi Mawu Oti ‘Adye Zonona’ (Ne 8:10) Sakutsutsana ndi Oti ‘Asamadye Mafuta’? (Le 3:17), 12/15
Kodi Mfumu Solomo Inali ndi Golide Wochuluka Bwanji? 11/1
Kodi Mfundo Yoti Zamoyo Zinachita Kusanduka Ndi Yogwirizana ndi Baibulo? 1/1
Kodi Mphamvu ‘Yochiritsa Mozizwitsa’ Masiku Ano Imachokera kwa Mulungu? 12/1
Kukula kwa Thawale la Pakachisi, 2/1
Kodi Yeriko Unali Mzinda Umodzi Kapena Iwiri? 5/1
‘Kuika Manja’ (Ahe 6:2), 9/15
Kusunga Misozi M’nsupa, 10/1
Kuwerenga Mpukutu, 4/1
Kuwonongedwa kwa Sodomu ndi Gomora, 3/1
Khoma Lenileni? (Aef 2:11-15), 7/1
Madzi Opatsa Moyo Wosatha, 6/1
Mafuta Onunkhira Amene Mariya Anagwiritsira Ntchito, 5/1
Mafuko 12 a Isiraeli Kapena 13? 7/1
Maliko Sanafooke, 2/1
Miyala ya Kachisi, 8/1
Mkwiyo wa Kaini, 7/1
Mtendere wa Mumtima, 2/1
Mwambo wa Ukalisitiya, 4/1
Munthu Amene Mumam’konda Akamwalira, 7/1
N’chifukwa Chiyani Ayuda Ankayamba Madzulo Kusunga Sabata? 10/1
N’chifukwa Chiyani Ayuda M’nthawi ya Yesu Anali Omwazikana? 11/1
N’chifukwa Chiyani Davide Sanachite Mantha? 12/1
N’chifukwa Chiyani Zekariya Analosera za Kuwonongedwa kwa Turo, Mzindawu Utawonongedwa Kale? 6/1
“Ndinetu Mdzakazi wa Yehova!” (Mariya), 7/1
Posachedwapa Dzikoli Likhala Paradaiso, 8/1
Sanasunthike Pakulambira Koona (Eliya), 1/1
Saulo anatchedwa liti Paulo? 3/1
Tel Arad, 7/1
Timakobili Tiwiri ta Mkazi Wamasiye, 3/1
Timoteyo, 4/1
Ufumu wa Mulungu, 1/1, 5/1
“Ulendo wa Tsiku la Sabata,” 10/1
Zochitika mu Lydia Zimatikhudza, 4/1
“Zombo za ku Tarisi,” 11/1
YEHOVA
Amaona Kuti Ndife Ofunika Kwambiri, 4/1
Amene Angabwezeretse Moyo, 3/1
Atate Yemwe Alibe Wofanana Naye, 1/1
‘Dzina Losafunika Kulitchula’? 6/1
“Ilitu Ndi Dzina Loyera Ndiponso Lalikulu la Mulungu,” 10/15
Iye Amamvetsa Mavuto Athu, 5/1
“Iye Sali Kutali ndi Aliyense wa Ife,” 7/1
Khalani mu Gulu la Ana a Mulungu, 3/1
“Khalani Otsanzira Mulungu,” 10/1
Kodi Chilengedwe Chimasonyeza Chiyani Ponena za Mulungu? 5/1
Kodi Dzinali Liyenera Kupezeka mu Chipangano Chatsopano? 8/1
Kodi Amavomereza Kulambira Kwina Kulikonse? 6/1
Kodi Mumawadziwa Atate Wanu wa Kumwamba? 9/1
Kodi N’chiyani Chingathe “Kutilekanitsa ndi Chikondi cha Mulungu”? 8/1
Kodi N’kulakwa Kugwiritsa Ntchito Dzina la Mulungu? 7/1
Masoka Achilengedwe Chilango Chochokera kwa Mulungu? 5/1
M’busa Amene Amakusamalirani, 2/1
Mlengi Woyenera Kulandira Ulemerero, 12/1
Mulungu Amakhululuka, 6/1
“Mulungu wa Chitonthozo Chonse,” 9/1
N’chifukwa Chiyani Amalola Kuti Tizivutika? 2/1
Ngati Katchulidwe ka Sikadziwika Bwinobwino, Tiyenera Kuligwiritsira Ntchito? 9/1
Wokonda Chilungamo, 11/1
Yesu ndi Petulo Anangopereka Ndalama Imodzi pa Msonkho wa Pakachisi, 2/1
Zimene Tikuphunzira kwa Yesu, 2/1
Zimene Yehova Amalosera, 1/1
YESU KHRISTU
Anagometsa Anthu, 9/1
Ankalankhula Chinenero Chanji? 8/1
Anali Kunena za Moto wa Helo? (Mko 9:48), 6/15
Anachiritsa Anthu Mozizwitsa, 5/1
Anachiritsa Munthu Wosaona Mwapang’onopang’ono, 4/1
Kuneneratu za Mesiya, 10/1
Kodi imfa ya Yesu Ingatipulumutse Bwanji? 3/1
Kodi Mumatsanzira Yesu Pamoyo Wanu? 12/1
,N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera M’dzina la Yesu? 2/1
N’chifukwa Chiyani Yudasi Anapatsidwa Ndalama 30 Zasiliva? 9/1
N’chifukwa Chiyani Anatenga Masiku Anayi Asanafike ku Manda a Lazaro? 1/1
Nchito ya Ukalipentala, 12/1
“Mulungu” Kapena “mulungu”? 11/1
Mmene Tiyenera Kukhalira ndi Ena, 8/1
Okhulupirira Nyenyezi Anakamuona Liti? 1/1
“Osunga Ndalama” Amene Anawatchula, 12/1
Pontiyo Pilato Anachita Mantha Atamva kuti Yesu “Akudziyesa Yekha Mwana wa Mulungu,” 6/1
Petulo Akana Yesu, 1/1