Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zamkatimu

Zamkatimu

Zamkatimu

November 15, 2009

Magazini Yophunzira

NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:

December 28, 2009–January 3, 2010

Kodi Mapemphero Anu Amasonyeza Chiyani za Inuyo?

TSAMBA 3

NYIMBO ZOIMBA: 51, 13

January 4-10, 2010

Kuphunzira Baibulo Kungathandize Kuti Mapemphero Anu Azikhala Atanthauzo

TSAMBA 7

NYIMBO ZOIMBA: 6, 22

January 11-17, 2010

Yamikirani Malo Anu Mumpingo wa Mulungu

TSAMBA 13

NYIMBO ZOIMBA: 53, 48

January 18-24, 2010

Pitirizani Kukulitsa Chikondi Chanu Chaubale

TSAMBA 20

NYIMBO ZOIMBA: 25, 50

January 25-31, 2010

Tiyenera Kukhala Aulemu Popeza Ndife Atumiki a Mulungu

TSAMBA 24

NYIMBO ZOIMBA: 34, 3

Cholinga cha Nkhani Zophunzira

Nkhani Zophunzira 1 ndi 2 TSAMBA 3-11

Pa nkhani ziwirizi, yoyamba ikuthandizani kuonanso bwino mapemphero anu kwa Yehova. Yachiwiri ikulimbikitsani kuti muziwerenga bwinobwino mapemphero ndiponso mawu otamanda ndi kuyamika Mulungu amene analembedwa m’Baibulo, ndipo kuchita zimenezi kungakuthandizeni kudziwa zimene mungachite kuti mapemphero anu azikhala atanthauzo.

Nkhani Yophunzira 3 TSAMBA 13-17

Mkhristu aliyense ali ndi malo ake mumpingo wa Yehova. Nkhaniyi ikufotokoza njira zosiyanasiyana zimene tingasonyezere kuti timayamikira malo athu mumpingo wachikhristu.

Nkhani Zophunzira 4, 5 TSAMBA 20-29

Kusonyeza chikondi chaubale n’kofunika kwambiri kuti mumpingo mukhale mgwirizano. Ndipo ulemu ndi wofunika kwambiri mu utumiki wakumunda. Nkhanizi zikusonyeza mmene tingakulitsire makhalidwe awiriwa pa moyo wathu.

M’MAGAZINI INO MULINSO:

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

TSAMBA 12

Kupereka Mokondwera Kuchokera Pansi pa Mtima

TSAMBA 18

Kamtsikana Kowolowa Manja

TSAMBA 29

Muziona Kuti Abale ndi Alongo Anu Osamva Ndi Ofunika Kwambiri

TSAMBA 30