Zamkatimu
Zamkatimu
July 15, 2011
Magazini Yophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA MILUNGU YA:
August 29, 2011–September 4, 2011
Kodi Mukutsatira Malangizo Achikondi a Yehova?
TSAMBA 10
NYIMBO ZOIMBA: 26, 3
September 5-11, 2011
Kodi Mukutsatira Machenjezo a Yehova Omveka Bwino?
TSAMBA 15
NYIMBO ZOIMBA: 32, 52
September 12-18, 2011
Kodi Mpumulo wa Mulungu N’chiyani?
TSAMBA 24
NYIMBO ZOIMBA: 19, 27
September 19-25, 2011
Kodi Mwalowa mu Mpumulo wa Mulungu?
TSAMBA 28
NYIMBO ZOIMBA: 55, 24
Cholinga cha Nkhani Zophunzira
NKHANI ZOPHUNZIRA 1, 2 TSAMBA 10-19
Yehova amatichenjeza mwachikondi za zinthu zoipa zimene zingatisocheretse pa njira yopita ku moyo wosatha. Nkhani ziwirizi zikufotokoza zinthu 6 zimene zingatisocheretse ndiponso mmene tingazipewere.
NKHANI ZOPHUNZIRA 3, 4 TSAMBA 24-32
Baibulo limanena kuti Yehova atalenga anthu “anapuma” pa tsiku la 7. (Aheb. 4:4) Pa nkhani ziwirizi, yoyamba ikufotokoza cholinga cha tsiku la mpumulo wa Mulungu ndiponso chifukwa chake lili lofunika kwa ife. Nkhani yachiwiri ikufotokoza njira zina zimene tingasonyezere kuti talowa nawo mu mpumulo wa Yehova.
M’MAGAZINI INO MULINSO NKHANI IZI
3 Nsanja ya Olonda Yatsopano ya M’Chingelezi Chosavuta
4 Anthu a Yehova Awina Milandu Imene Yatenga Nthawi Yaitali
20 Ndinkaopa Imfa Koma Tsopano Ndikuyembekezera ‘Moyo Wochuluka’