Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2011
Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2011
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
Kodi Mumasangalala Kuwerenga? 5/15
Kodi Nthawi Ankaitchula Bwanji? 5/1
Limasintha Anthu, 2/1, 4/1, 5/1, 7/1, 8/1, 10/1, 11/1
Linalembedwa Liti, 6/1
Maulosi 6 a M’Baibulo Amene Akukwaniritsidwa, 5/1
Olivétan—‘Anamasulira,’ 9/1
Pa Anthu Olemba Malemba Achigiriki, ndi Ati Amene Analipo pa Pentekosite? 12/1
Zamora Anayesetsa Kumasulira Molondola, 12/1
Zoti Achinyamata Achite, 1/1, 3/1, 5/1, 7/1, 9/1, 11/1
MBIRI YA MOYO WANGA
Kutumikira Yehova Kwandibweretsera Chimwemwe (F. Rusk), 10/15
Kutumikira Yehova Ngakhale pa Nthawi Zovuta (M. de Jonge-van den Heuvel), 1/15
Kuwerenga Baibulo Kwandilimbikitsa pa Moyo Wanga Wonse (M. Leroy), 9/15
Ndapeza Zinthu Zambiri Zabwino (A. Bonno), 4/15
Ndapindula Kwambiri Chifukwa Chololera Kusintha Zinthu (J. Thompson), 12/15
Ndinkafunitsitsa Ntchito Yoyenda M’madera Osiyanasiyana (Z. Dimitrova), 6/1
Ndinkaopa Imfa Koma Tsopano Ndikuyembekezera ‘Moyo Wochuluka’ (P. Gatti), 7/15
Ngati Mwana wa Yefita (J. Soans), 12/1
“Panopa Ndine Wolumala, Koma Sindidzakhala Chonchi Mpaka Kalekale” (S. van der Monde), 11/15
“Woyang’anira Wabwino Ndiponso Mnzathu Wapamtima” (J. Barr), 5/15
MBONI ZA YEHOVA
“Anthu Olimba Mtima Ofunika Kuwayamikira” (Germany), 10/1
Kalata Yochokera ku . . . , 3/1, 6/1, 9/1, 12/1
Kodi Amalandira Chithandizo Chachipatala? 2/1
Kuwina Milandu Imene Yatenga Nthawi Yaitali (Russia), 7/15
Kuyesetsa Kuti Anthu Asaipitse Mbiri Yawo (Russia), 5/1
Misonkhano Yachigawo ku Russia, 3/1
Misonkhano Yachigawo yakuti, “Ufumu wa Mulungu Ubwere,” 6/1
Msonkhano Wapachaka, 8/15
Mwambo Womaliza Maphunziro a Giliyadi, 2/1, 8/1
“Mwayi Wopereka Nawo Mphatso Zachifundo” (zopereka), 11/15
Nsanja ya Olonda ya M’Chingelezi Chosavuta, 7/15
Zinthu Zimene Mungakondwere Nazo (gulu la Mulungu), 3/15
Ziwerengero za mu Lipoti la Chaka Chautumiki, 8/15
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Abambo Azigwirizana ndi Ana Awo Aamuna, 11/1
Banja Lanu Lizikonda Zinthu Zauzimu, 11/1
Funso Kapena Ngati Ndili ndi Vuto, 10/15
Khalani Olimba Mtima Ngati Pinihasi, 9/15
Khalanibe Oona Mtima M’dziko la Anthu Osaona Mtima, 4/15
Kodi Achinyamata Ayenera Kubatizidwa? 6/15
Kodi Makolo Aziphunzitsa Ana Awo Nkhani Zokhudza Kugonana? 11/1
Kodi Mumayamikira Madalitso Amene Muli Nawo? 2/15
Kugwiritsa Ntchito Intaneti, 8/15
Kukhala ndi “Moyo Wopambana,” 6/15
‘Kukhalabe Maso,’ 10/15
Kulambira kwa Pabanja, 8/15
“Kumvera Kuposa Nsembe,” 2/15
Misonkho, 9/1
Mungatani Kuti Banja Lanu Likhale Lolimba? 2/1
Mungatani Kuti Banja Lanu Likhale Losangalala? 10/1
Musadzinyenge ndi Maganizo Onama, 3/15
Musalole Kuti Matenda Akulandeni Chimwemwe, 12/15
Musasiye Okhulupirira Anzanu, 3/15
Muziganizira Zimene Yehova Wakuchitirani Kale, 1/15
Muzilemekeza Mwamuna Kapena Mkazi Wanu, 8/1
Muziphunzitsa Ana Anu Makhalidwe Abwino, 2/1
‘Nthawi ya Chikondi, Nthawi ya Chidani,’ 12/1
Phunzitsani Ana Anu, 2/1, 4/1, 6/1, 8/1, 10/1, 12/1
Phunzitsani Ana Anu Ulemu, 2/15
Tingapeze Bwanji Anzathu Abwino? 12/1
Tiyenera Kuchita Khama (Kulambira kwa Pabanja), 2/15
Tiyeni Tisangalale Limodzi, 10/15
Umboni Wakuti Mulungu Akutitsogolera, 4/15
Zinthu Zimasintha M’banja Mukabadwa Mwana, 5/1
NKHANI ZOPHUNZIRA
Anapeza Mesiya, 8/15
Anthu Amene Amakhulupirira Yehova Amakhala Olimba Mtima, 5/15
Anthu Ankayembekezera Mesiya, 8/15
Anthu Okhulupirika Akale Amene Anatsogoleredwa ndi Mzimu wa Mulungu, 12/15
Anthu Ovomerezeka ndi Mulungu Adzapeza Moyo Wosatha, 2/15
Khalani Okonzeka, 3/15
Khalani Tcheru Ngati Yeremiya, 3/15
Khulupirirani Yehova, “Mulungu Amene Amatitonthoza M’njira Iliyonse,” 10/15
Kodi Mpumulo wa Mulungu N’chiyani? 7/15
Kodi Mukulola Mzimu wa Mulungu Kukutsogolerani? 4/15
Kodi Mukulola Yehova Kukhala Cholowa Chanu? 9/15
Kodi Mukutsatira Machenjezo a Yehova Omveka Bwino? 7/15
Kodi Mukutsatira Malangizo Achikondi a Yehova? 7/15
Kodi Mumadana Ndi Kusamvera Malamulo? 2/15
Kodi Mumadziwika ndi Yehova? 9/15
Kodi Munthu Wofunika Kwambiri pa Moyo Wanu Ndi Ndani? 5/15
Kodi Mwalowa mu Mpumulo wa Mulungu? 7/15
Kodi Solomo Ndi Chitsanzo Chabwino Kapena Choipa? 12/15
Kodi Zimene Mumachita pa Nthawi Yosangalala Zimakhala Zopindulitsa? 10/15
Landirani Mzimu wa Mulungu Osati wa Dziko, 3/15
Mabanja Achikhristu Ayenera ‘Kukhala Okonzeka,’ 5/15
Mabanja Achikhristu Ayenera ‘Kukhalabe Maso,’ 5/15
“Makhalidwe Amene Mzimu Woyera Umatulutsa” Amalemekeza Mulungu, 4/15
Malangizo Anzeru kwa Anthu Amene Sali Pabanja Ndiponso Amene Ali Pabanja, 10/15
Mulungu Akuonetsa Chikondi Chake kwa Ife, 6/15
Muzidalira Yehova Pamene Mapeto Akuyandikira, 3/15
Muzigwiritsa Ntchito Mwanzeru Nthawi Imene Simuli pa Banja, 1/15
Muzikonda Chilungamo ndi Mtima Wanu Wonse, 2/15
“Muzilemekeza Anthu Amene Akugwira Ntchito Mwakhama Pakati Panu,” 6/15
Muzilemekeza Ukwati Monga Mphatso Yochokera kwa Mulungu, 1/15
Mzimu wa Mulungu Unkatsogolera Akhristu Oyambirira Ndipo Ukutsogoleranso Akhristu Masiku Ano, 12/15
Mzimu Woyera Umatipatsa Mphamvu Yolimbana ndi Mayesero Ndiponso Zofooketsa, 1/15
Mzimu Woyera Umatipatsa Mphamvu Yolimbana ndi Vuto Lililonse, 1/15
Mzimu Woyera Unagwira Ntchito Polenga Zinthu, 2/15
N’chifukwa Chiyani Tiyenera kutsogoleredwa ndi Mzimu wa Mulungu? 12/15
Ndife “Osakhalitsa” M’dziko Loipali, 11/15
‘Nzeru za Mulungu N’zozama’ Kwambiri (Aroma 11), 5/15
Pali Uthenga Wabwino Wofunika Kuti Anthu Onse Amve, 6/15
‘Pezani Chitetezo M’dzina la Yehova,’ 1/15
‘Thamangani N’cholinga Choti Mukalandire Mphoto,’ 9/15
Thandizani Amuna Kukula Mwauzimu, 11/15
Thandizani Ena Kuti Ayenerere Maudindo, 11/15
Tiyeni Tithamange Mpikisano Mopirira, 9/15
Tiziona Kuti Kutumikira Yehova Ndi Chinthu Chofunika Kwambiri, 4/15
‘Tonthozani Anthu Onse Olira,’ 10/15
“Usadalire Luso Lako Lomvetsa Zinthu,” 11/15
“Wetani Gulu la Nkhosa za Mulungu Lomwe Analisiya M’manja Mwanu,” 6/15
Yehova Ndi Cholowa Changa, 9/15
Yehova Ndi “Mulungu Amene Amapatsa Mtendere,” 8/15
Yendani Mogwirizana ndi Mzimu Kuti Mupeze Moyo ndi Mtendere, 11/15
Yesetsani Kukhala pa Mtendere ndi Ena, 8/15
Zosankha Zanu Zizilemekeza Mulungu, 4/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
“A M’nyumba ya Kaisara” (Afil. 4:22), 3/1
“Akazi Ambiri” (Mlal. 2:8), 3/15
Anakhalabe Wokhulupirika Ngakhale Anakumana ndi Mavuto (Samueli), 1/1
Analimba Mtima Kuteteza Anthu a Mulungu (Esitere), 10/1
Analimbikitsidwa ndi Mulungu (Eliya), 7/1
Anthu Osintha Ndalama M’kachisi, 10/1
Atumwi Anatenga Ndodo N’kuvala Nsapato, 3/15
Baraba, 4/1
“Chikondwerero cha kupereka kachisi kwa Mulungu” (Yohane 10:22), 9/1
“Dziko Loyenda Mkaka ndi Uchi,” 3/1
Kodi Abulahamu Analidi ndi Ngamila? 6/15
Kodi Akhristu Onse Okhulupirika Amapita Kumwamba? 6/1
Kodi Akufa Adzauka? 6/1
Kodi Amene Akulamulira Dzikoli Ndani? 9/1
Kodi Aramagedo N’chiyani? 9/1
Kodi Atsogoleri Achipembedzo Achiyuda Ankawaona Bwanji Anthu Wamba? 7/1
Kodi Chipembedzo Choona Mungachidziwe bwanji? 8/1
Kodi Dzikoli Litha mu 2012? 12/1
Kodi Gehena Ndi Malo Amene Anthu Amakapsa? 4/1
Kodi Masoka Achilengedwe Ndi Chilango? 12/1
Kodi Moyo Wosatha Udzafika Potopetsa? 5/1
Kodi Mukukonzekera Tsiku Lofunika Kwambiri? 2/1
Kodi Munthu Ankaphedwa Ngati Yesu Akapalamula Mlandu Wotani? 4/1
Kodi N’chifukwa Chiyani Satana Anagwiritsa Ntchito Njoka? 1/1
Kodi N’chifukwa Chiyani Solomo Anaitanitsa Mitengo ku Lebanoni? 2/1
Kodi Ndani Angamasulire Ulosi? 12/1
Kodi Papa Ndi Wolowa M’malo mwa Petulo? 8/1
Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani? 7/1
Kodi Ufumu wa Mulungu Uli Mumtima? 3/1
Kodi Yerusalemu Anawonongedwa Liti? 10/1, 11/1
Kubatiza Ana Akhanda, 10/1
Kudziwa Nthawi Usiku, 8/1
Kugula Zinthu Mogwirizana ndi Ndalama, 6/1
‘Kumenya Zisonga Zotosera’ (Mac. 26:14), 8/1
Kupeza Madzi M’nyengo ya Chilimwe ku Isiraeli, 1/1
Kutchova Juga, 3/1
Kuthetsa Umphawi, 6/1
Lamulo Lokhudza Khunkha, 2/1
Mayina Odindidwa pa Zomatira Zadongo, 5/1
Mitengo ya Maolivi Ankaiona Kuti Ndi Yofunika , 10/1
“Mitundu 7 ya Mbewu” M’dziko Labwino, 9/1
Moyo Waphindu, 7/1
Munda wa Edeni, 1/1
Munthu wa Kum’mawa kwa Asia Anapezeka ku Italy, 1/1
Munthu Wapamtima pa Yehova, 9/1
N’chifukwa Chiyani Mose Anakwiyira Ana a Aroni? (Lev. 10:16-20), 2/15
Ndalama (Moyo wa anthu akale), 5/1
Ndalama Zoyendetsera Ntchito Zapakachisi, 11/1
“Ndimakhulupirira” (Malita), 4/1
Nyumba Imene Abulamu Ankakhala, 1/1
Petulo Anali Kunyumba ya Wofufuta Zikopa, 6/1
Tanthauzo la dzina loti Kaisara, 7/1
Ukwati Wapachilamu Kapena Kuti Wolowa Chokolo, 3/1
“Ulusi Wofiira Kwambiri,” 12/1
‘Unditengerenso Mipukutu Makamaka Yazikopa,’ 6/15
‘Uthenga Wabwino wa Ufumu,’ 3/1
Yehu Anamenyera Nkhondo Kulambira Koyera, 11/15
Zimene Baibulo Limanena pa Nkhani ya Kugonana, 11/1
Zinthu Zimene Nebukadinezara Anamanga, 11/1
YEHOVA
Dzina lake M’chigwa (Switzerland), 1/15
Kodi Ali ndi Gulu Lake? 6/1
Kodi Ali ndi Malo Enieni Amene Amakhala? 8/1
Kodi Amakukondanidi? 1/1
Kodi Amaona Kuti Mtundu Wina Ndi Wofunika? 7/1
Kodi Ana Ayenera Kuphunzitsidwa Chiyani? 8/1
Kodi Anadziwiratu Kuti Adamu ndi Hava Adzachimwa? 1/1
Kodi Analenga Mdyerekezi? 3/1
Kodi Analengeranji Dziko Lapansi? 4/1
Kodi Mulungu Ndani? 2/1
Malamulo a Zinthu Zakuthambo, 7/1
Malamulo Ake Amatithandiza, 11/1
N’Chifukwa Chiyani Ankapatsa Aisiraeli Zinziri? 9/1
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzitsidwa Naye? 1/1
N’chifukwa Chiyani Walola Kuti Zoipa Zizichitika? 5/1
Yandikirani Mulungu, 1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 7/1, 8/1, 9/1, 10/1, 11/1, 12/1
Zikhulupiriro Zisanu Zabodza, 10/1
YESU KHRISTU
Anaweruzidwa Mopanda Chilungamo, 4/1
Chiwerengero cha Maulosi Onena za Mesiya, 8/15
Kodi Anachokera Kuti; Anachita Zotani; N’chifukwa Chiyani Anafa? 4/1
Kodi Anafera Pamtanda? 3/1
Kodi Yesu Khristu Ndani? 3/1
Mawu akuti “Mwanena Nokha,” 6/1
Nthawi Imene Anapachikidwa, 11/15
Tsatirani Khristu Yemwe Ndi Mtsogoleri Wabwino Kwambiri, 5/15