Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Yehova Anaulula Mafumu 8

Yehova Anaulula Mafumu 8

Yehova Anaulula Mafumu 8

Mabuku a m’Baibulo a Danieli ndiponso Chivumbulutso amaulula mafumu 8, kapena kuti maulamuliro 8 a anthu. Amasonyezanso nthawi imene maulamulirowo adzaonekera. Kumvetsa ulosi woyambirira wa m’Baibulo kungatithandize kumvetsanso maulosi a m’buku la Danieli ndiponso Chivumbulutso amenewa.

Kuyambira kalekale, Satana anakonza zoti mbewu yake izikhala ndi maufumu kapena maboma. (Luka 4:5, 6) Koma ndi maufumu ochepa okha padziko lapansi amene alowerera kwambiri m’zochita za anthu a Mulungu, omwe ndi Aisiraeli ndiponso Akhristu odzozedwa. Masomphenya a Danieli ndi Yohane amafotokoza maulamuliro 8 okha amene achita zimenezi.

[Tchati/​Zithunzi pamasamba 12, 13]

(Onani m’magazini yeniyeni kuti mumvetse izi)

MAULOSI A MAULOSI A M’BUKU

M’BUKU LA DANIELI LA CHIVUMBULUTSO

1. Iguputo

2. Asuri

3. Babulo

4. Mediya ndi

Perisiya

5. Girisi

6. Roma

7. Britain ndi

United States *

8. Mabungwe a League of Nations

ndi United Nations *

ANTHU A MULUNGU

2000 B.C.E.

Abulahamu

1500

Mtundu wa Isiraeli

1000

Danieli 500

B.C.E./​C.E.

Yohane

Isiraeli wa Mulungu 500

1000

1500

2000 C.E.

[Mawu a M’munsi]

^ ndime 13 Mafumu onsewa akhalapo nthawi ya mapeto. Onani tsamba 19.

^ ndime 14 Mafumu onsewa akhalapo nthawi ya mapeto. Onani tsamba 20.

[Zithunzi]

Chifaniziro chachikulu (Dan. 2:31-45)

Zilombo zinayi zimene zinatuluka m’nyanja (Dan. 7:3-8, 17, 25)

Nkhosa yamphongo ndi mbuzi (Dan. 8)

Chilombo cha mitu 7 (Chiv. 13:1-10, 16-18)

Chilombo cha nyanga ziwiri chinalimbikitsa anthu kupanga chifaniziro cha chilombo (Chiv. 13:11-15)

[Mawu a Zithunzi]

Photo credits: Egypt and Rome: Photograph taken by courtesy of the British Museum; Medo-Persia: Musée du Louvre, Paris