Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2012
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
Baibulo la Chingelezi la Coverdale, 6/1
Kodi Limalosera Zam’tsogolo? 1/1
Kuligwiritsa Ntchito Ngati Chithumwa, 12/15
La Chiswahili, 9/1
Limasintha Anthu, 1/1, 2/1, 4/1, 5/1, 7/1, 8/1, 10/1, 11/1
N’losiyana ndi Mabuku Ena, 6/1
Zoti Achinyamata Achite, 1/1, 4/1, 7/1, 10/1
MBIRI YA MOYO WANGA
“Chinsinsi” Chimene Taphunzira Potumikira Mulungu (O. Randriamora), 6/15
“Kudzanja Lamanja Kuli Chimwemwe” (L. Didur), 3/15
Mawu a Mulungu Anathandiza Banja Lachihindu (N. Govindsamy), 10/1
Ndagwira Chovala cha Myuda kwa Zaka 70 (L. Smith), 4/15
Ndinapeza Ufulu Weniweni (M. Kilin), 12/1
Ndinkacheza ndi Achikulire Anzeru (E. Gjerde), 5/15
Tsopano Ndikudziwa Mulungu Amene Ndikum’tumikira (M. Bacudio), 9/1
Ubwenzi wa Zaka 60 (L. Turner, W. Kasten, R. Kelsey, R. Templeton), 10/15
Yehova Anandiphunzitsa Kuchita Chifuniro Chake (M. Lloyd), 7/15
Yehova Watsegula Maso Anga (P. Oyeka), 6/1
MBONI ZA YEHOVA
Aaziteki, 3/1
Akopotala, 5/15
Anadzipereka ku Brazil, 10/15
Anadzipereka ku Ecuador, 7/15
‘Anali Asanamvepo Uthenga Wabwino’ (wailesi ku Canada), 11/15
Ankalalikira Mawu a Mulungu Molimba Mtima, 2/15
Kalata Yochokera . . . , 3/1, 6/1, 9/1, 12/1
‘Kankachititsa Kuti Ndizionekera Patali’ (kanjinga), 2/15
Khoti Linagamula za Ufulu Wokana Usilikali (V. Bayatyan), 11/1
Kodi Akazi Amaphunzitsa Mawu a Mulungu? 9/1
“Kodi Mungatijambule?” (Mexico), 3/15
‘Kodi Ndingakwanitse Kulalikira?’ (wolumala), 1/15
Kukomera Mtima Munthu Wokwiya Kumathandiza, 6/15
Kusunga Zinthu Zathu Zamtengo Wapatali, 1/15
Magazini Yophunzira (Nsanja ya Olonda), 1/15
Mawu a “Ana Aang’ono” (Russia, Australia), 10/15
Misonkhano Yachigawo Yakuti ‘Tetezani Mtima Wanu,’ 5/1
Msonkhano Wapachaka, 8/15
Mwambo wa Omaliza Sukulu ya Giliyadi, 2/1, 8/1
N’chifukwa Chiyani Timalalikira Kunyumba ndi Nyumba? 6/1
Nsanja ya Olonda ya M’Chingelezi Chosavuta, 12/15
Ogwirizana M’mayiko Osiyana (Portugal, Spain, France), 1/1
Oyang’anira Oyendayenda Akale, 8/15
Sukulu Zophunzitsa Atumiki a Mulungu, 9/15
“Zimene Ndinkafuna Zatheka” (upainiya), 7/15
Zimene Zinachitika ku Estonia, 12/1
Zochuluka Zinathandiza Osowa (zopereka), 11/15
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
Chikalata Cholumbira Kukhulupirika mu Ukwati, 12/15
Kodi Akhristu a M’nthawi ya Atumwi Ankachita Nawo Ndale? 5/1
Kodi Banja Limapangitsa Munthu Kukhala Wosangalala? 10/1
Kodi Mkhristu Angachotsedwe Chifukwa Choonera Zolaula? 3/15
Kodi Mumatani Ena Akakupemphani Malangizo? 3/15
Kukoma Mtima, 9/1
Kupindula ndi Kusangalala Mukamaphunzira, 1/15
Mphatso Yokhala Wosakwatira, 11/15
Muzifufuza “Nzeru Zoyendetsera Moyo,” 6/15
Mwana Wanu Akayamba Kukayikira Chipembedzo, 2/1
N’chifukwa Chiyani Akhristu Amabatizidwa? 4/1
Ngongole, 11/1
Phunzitsani Ana Anu, 3/1, 6/1, 9/1, 12/1
“Samalani ndi Chofufumitsa cha Afarisi,” 5/15
Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo, 2/1, 5/1, 8/1, 11/1
NKHANI ZOPHUNZIRA
Akhristu Oona Amalemekeza Mawu a Mulungu, 1/15
‘Anatsogoleredwa ndi Mzimu Woyera,” 6/15
Ansembe Achifumu Amene Adzapindulitse Anthu Onse, 1/15
“Anthu Osakhalitsa M’dzikoli” Ndi Ogwirizana Polambira Mulungu, 12/15
“Ine Ndili Pamodzi ndi Inu,” 8/15
‘Khalani Olimba Mtima Kwambiri Ndipo Muchite Zinthu Mwamphamvu,’ 2/15
Khalanibe Odzipereka, 3/15
Khulupirirani Yehova, Mulungu wa “Nthawi ndi Nyengo,” 5/15
Kodi Dzikoli Lidzatha Bwanji? 9/15
Kodi Mukuonetsa Ulemerero wa Yehova? 5/15
Kodi Mumaika Kutumikira Yehova pa Malo Oyamba? 6/15
Kodi Mumaonetsa Mzimu Wotani? 10/15
Kusakhulupirika Ndi Chizindikiro cha Masiku Otsiriza, 4/15
Limbani Mtima Pokumana ndi Mavuto, 10/15
Lolani Yehova Kukutsogolerani ku Ufulu Weniweni, 7/15
Mtendere Udzayamba mu Ulamuliro wa Zaka 1,000, 9/15
Mukati Inde Akhaledi Inde, 10/15
Mukhoza Kukhala ndi Moyo Wabwino Kwambiri, 12/15
Musamayang’ane “Zinthu za M’mbuyo,” 3/15
Musasunthike Popewa Misampha ya Satana, 8/15
Musataye Mtima Ngati Banja Lanu Silikuyenda Bwino, 5/15
Muzichita Zinthu Monga Nzika za Ufumu, 8/15
Muzikhululukirana ndi Mtima Wonse, 11/15
Muziyamikira Mphatso ya Ukwati Yochokera kwa Mulungu, 5/15
Mverani Mulungu Kuti Mupindule ndi Malumbiro Ake, 10/15
‘Mwana Amakonda Kuululira Ena za Atate,’ 4/15
“Ndingachitenso Mantha ndi Ndani?” 7/15
Ndinu Mtumiki Wokhulupirika, 12/15
“Ndiphunzitseni Kuchita Chifuniro Chanu,” 11/15
N’zotheka Kukhala Osangalala M’banja Limene Wina Si Mboni, 2/15
Phunzirani Kuchokera ku Choonadi cha M’chilamulo, 1/15
Phunzirani Kukhala Maso Kuchokera kwa Atumwi a Yesu, 1/15
Pitirizani Kukhala Monga “Anthu Osakhalitsa M’dzikoli,” 12/15
Pitirizani Kutumikira Yehova ndi Mtima Wathunthu, 4/15
Samalani ndi Misampha ya Mdyerekezi, 8/15
“Simukudziwa Tsiku Kapena Ola Lake,” 9/15
Thandizani Anthu Kuti ‘Adzuke ku Tulo,’ 3/15
Thandizani Mpingo Kukhalabe ndi Maganizo Abwino, 2/15
Tizipereka Nsembe kwa Yehova ndi Moyo Wathu Wonse, 1/15
Tizisangalala ndi Chiyembekezo Chathu, 3/15
Tsanzirani Kuleza Mtima kwa Yehova ndi Yesu, 9/15
Tsanzirani Yesu pa Nkhani Yokhala Maso, 2/15
Tumikirani Mulungu Amene Amapereka Ufulu, 7/15
Yehova Akusonkhanitsa Banja Lake, 7/15
Yehova Amadziwa Kupulumutsa Anthu Ake, 4/15
Yehova Amasonkhanitsa Anthu Ake Osangalala, 9/15
Yehova Amatiteteza Kuti Tidzapulumuke, 4/15
Yehova Ndi Wofunitsitsa Kukukhululukirani, 11/15
Yehova Ndi “Woulula Zinsinsi,” 6/15
Yehova Waulula “Zimene Ziyenera Kuchitika Posachedwapa,” 6/15
Yesetsani Kukhala Ngati Wamng’ono, 11/15
Yesu Anatipatsa Chitsanzo cha Kudzichepetsa, 11/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Abulahamu, 1/1
Ahasiwero (m’buku la Esitere), 1/1
Akhristu Anathawa mu Yudeya Chaka cha 70 C.E Chisanafike, 10/1
“Ana a Aneneri,” 10/1
Anachita Zinthu Mwanzeru, Molimba Mtima, Moganizira Ena (Esitere), 1/1
Anasi wa M’Mauthenga Abwino, 4/1
Ankateteza ndi Kusamalira Banja Lake (Yosefe), 4/1
Aramagedo, 2/1
Chipembedzo Ndiponso Ndale, 5/1
Fodya, 8/1
Guwa la “Mulungu Wosadziwika,” 3/1
Imfa ya Okhulupirika a Yehova “Ndi Nkhani Yaikulu,” 5/15
Inki ndi Zolembera Zakale, 11/1
Kaduka, 2/15
Kodi Abwino Amapita Kumwamba? 8/1
Kodi Anthu Ankaimba Zitoliro pa Maliro? 2/1
Kodi Anthu Ankatumiza Bwanji Makalata? 9/1
Kodi Dziko Lapansili Lidzawonongedwa? 2/1
Kodi Kukhala ndi Chikhulupiriro N’kusaganiza Bwino? 11/1
Kodi Mchere Umatha Mphamvu? (Mat. 5:13), 12/1
Kodi Mungawadziwe Bwanji Akhristu? 3/1
Kodi Musanabadwe Munakhalapo Kwinakwake? 12/1
Kodi N’zosathekadi? 6/1
Kodi N’zotheka Kukhala ndi Moyo Kwamuyaya? 10/1
Kodi Ziphuphu Zidzatha? 10/1
Kugwiritsa Ntchito Phula Ngati Matope, 7/1
Kugwiritsa Ntchito Vinyo Ngati Mankhwala, 8/1
Kukhulupirira Zamizimu, 3/1
“Kumene Inu Mupite Inenso Ndipita” (Rute), 7/1
Kupeza Ndalama Zochepa, 6/1
Kusunga M’firiji Mazira Amene Ayamba Kukula, 12/15
Kutaya Ndalama ya Dalakima, 12/1
Kuweruza Potengera Maonekedwe, 3/1
Kuyambiranso Kukhulupirirana (chigololo), 5/1
Mahema Omwe Mtumwi Paulo Ankapanga, 11/1
Mapepala pa Nthawi Imene Baibulo Linkalembedwa, 7/1
M’busa (anthu akale), 11/1
Mibadwo ya Makolo Achiyuda, 6/1
Miyala ya Pachovala cha Mkulu wa Ansembe, 8/1
“Mkazi Wabwino Kwambiri” (Rute), 10/1
Mlimi (anthu akale), 5/1
‘Mpando Woweruzira Milandu’ (Mac. 18:12), 5/1
“Mphoto Chifukwa cha Ntchito Yanu” (Asa), 8/15
Msodzi (anthu akale), 8/1
Mungadzakhale ndi Tsogolo Labwino, 5/1
Natani Ankalimbikitsa Kulambira Koona, 2/15
N’chifukwa Chiyani Ena Sachita Khirisimasi? 12/1
N’chiyani Chidzachitikire Zipembedzo? 5/1
Njerwa ku Iguputo Wakale, 1/1
Nsalu Zakale Komanso Mitundu Yake, 3/1
Oimba Nyimbo Komanso Zida Zawo (anthu akale), 2/1
Okhometsa Misonkho (m’nthawi ya atumwi), 3/1
Pali Zosangalatsa Kuposa Khirisimasi, 12/1
Pamene Britain ndi America Anakhala Ulamuliro wa 7, 6/15
Sankayenera Kukwatirana ndi Anthu a Mitundu Ina, 7/1
Tesalonika, 6/1
Tsiku la Chiweruzo, 9/1
Utatu, 3/1
Yehova Anaulula Mafumu 8, 6/15
Zamalonda mu Isiraeli, 9/1
Zochita za Angelo ndi Ziwanda Zimatikhudza, 7/1
Zodzoladzola za Anthu Akale, 12/1
Zozizwitsa, 8/1
YEHOVA
Amamva Mapemphero, 7/1
Atate, 7/1
Kodi Adzakhazikitsa Boma Lolamulira Dziko Lonse? 11/1
Kodi Amalanga Anthu Kumoto? 10/1
Kodi Amaona Kuti Akazi Ndi Otsika? 9/1
Kodi Mungam’funse Chiyani? 11/1
N’chifukwa Chiyani Ali ndi Gulu? 2/1
N’chifukwa Chiyani Anatumiza Yesu Padziko? 12/1
N’chifukwa Chiyani Anauza Abulahamu Kupereka Mwana Wake? 1/1
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kugwiritsa Ntchito Dzina Lake? 6/1
Yandikirani Mulungu, 1/1, 2/1, 3/1, 4/1, 5/1, 6/1, 7/1, 8/1, 9/1, 10/1, 11/1, 12/1
YESU KHRISTU
Ayuda Anakhumudwa ndi Mmene Yesu Anafera, 5/1
Kodi Anakhala Liti Mfumu? 8/1
Kodi Ankachita Nawo Ndale? 5/1
Kodi Tizikumbukira Bwanji Imfa ya Yesu? 3/1
Kodi Yesu Ndi Mulungu? 4/1
Mabuku Amene Ena Amati Ndi Mauthenga Abwino, 4/1
Mafunso Onena za Yesu, 4/1
Mlandu wa Amene Anapachikidwa Limodzi ndi Yesu, 2/1
Ndani Anatumiza Nyenyezi? 4/1
“Umunyamulire Mtunda wa Makilomita Awiri” (Mat. 5:41), 4/1