Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2014
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
MBIRI YA MOYO WANGA
MBONI ZA YEHOVA
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
NKHANI ZOPHUNZIRA
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kodi Apitiriza Kuwononga Dzikoli N’kufika Poti Silingakonzedwenso? 9/1
Kodi Malamulo Amene Mulungu Anapatsa Aisiraeli Anali Achilungamo? 9/1
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera Kuti Ufumu Ubwere? 10/1
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kupemphera, Tizipemphera Bwanji? 7/1
N’chifukwa Chiyani Zigawenga Ankazithyola Miyendo Akamazipha? 5/1
Nkhondo Yomwe Inasintha Dziko Lonse (Nkhondo Yoyamba ya Padziko Lonse), 2/1