Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Anthu akamapemphera kuti Ufumu wa Mulungu ubwere, kodi kwenikweni amakhala akupempha chiyani?

TSAMBA 5.

▪ Kodi mungatani kuti muphunzire kuganiza kaye musanalankhule?

TSAMBA 10.

▪ Kodi Mulungu anachititsa kuti anthu akhaleko mwa kuwasintha kuchokera ku zinthu zina?

TSAMBA 14.

▪ Kodi Eliya anali ndani, ndipo tingaphunzire chiyani kwa iye?

TSAMBA 18.

▪ Kodi tingatsimikize bwanji kuti maulosi a m’Baibulo sanalembedwe zinthu zomwe analoserazo zitachitika kale?

TSAMBA 22.

▪ N’chifukwa chiyani Yehova Mulungu ali Atate wabwino kwambiri kuposa wina aliyense?

TSAMBA 25.

▪ Kodi ndi zoona kuti anthu okhulupirira nyenyezi anabwera ndi mphatso kwa Yesu usiku umene iye anabadwa?

TSAMBA 31.