Tsamba 32
Tsamba 32
▪ Tchulani zifukwa zinayi zotsimikizira kuti zimene Baibulo limalonjeza n’zoona. Onani tsamba 8.
▪ Kodi muyenera kulankhula motani ndi wachinyamata amene samayankha mafunso anu? Onani tsamba 12.
▪ Kodi makolo angatani kuti aphunzitse ana awo kukhala anthu oyamikira? Onani tsamba 13.
▪ Kodi Yesu ankatchula dzina la Mulungu polalikira Ayuda anzake? Onani tsamba 19.
▪ Kodi n’chiyani chinachititsa kuti munthu wina wa ku Mexico, amene anali m’gulu la zigawenga zotchedwa Ana a Satana, asinthe kwambiri pa moyo wake? Onani tsamba 28.