Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi ndani amene adzamasulidwa ku helo? Onani tsamba 9.

▪ Kodi Yesu anayerekezera imfa ndi chiyani? Onani tsamba 17.

▪ Kodi ndi zinthu ziwiri ziti zimene mungachite kuti mulimbitse ukwati wanu? Onani tsamba 19 ndi 20.

▪ Kodi a Mboni za Yehova amakhulupirira kuti ndi okhawo amene adzapulumuke? Onani tsamba 28.

▪ Kodi mungamange bwanji chikhulupiriro chanu pathanthwe? Onani tsamba 29.