Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi kutsanzira Yesu kungatithandize bwanji kukhala anthu abwino komanso osangalala? Onani tsamba 4.

▪ Pali chifukwa chachikulu chiti chokhalira aukhondo kuposa kukhala ndi thanzi labwino? Onani tsamba 9.

▪ Kodi Akhristu oyambirira anathetsa bwanji vuto lawo lolalikira kwa anthu achigiriki? Onani tsamba 18.

▪ Kodi ena amachiritsa ‘mozizwitsa’ mwa mphamvu ya ndani? Onani tsamba 22.

▪ Kodi akatswiri awiri a sayansi anaona bwanji za kupeza yankho la mafunso onena za mmene chilengedwe chinayambira mwa kugwiritsa ntchito ndalama zokwana masenti 25? Onani tsamba 26.