Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi Baibulo ndi losiyana m’njira ziti ndi mabuku ena opereka amalangizo? Onani tsamba 4.

▪ Werengani za mavuto komanso zinthu zochititsa chidwi zimene zinachitikira anthu omasulira Baibulo m’zinenero zamakono. Onani tsamba 8.

▪ Kodi ndi zoona kuti zipembedzo zonse zimalambira Mulungu mmodzi yekha basi? Onani tsamba 12.

▪ Werengani za m’mene munthu wina anamvera atakalalikira uthenga wabwino ku dera lozizira kwambiri, kumpoto kwa Siberia. Onani tsamba 24.

▪ Kodi n’ndani amene angakutonthozeni ndiponso kukuthandizani mukakumana ndi mavuto? Onani tsamba 28.