Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi ndi ndani amene angakuthandizeni kuti mumvetse bwino Baibulo? Onani masamba 6 mpaka 8.

▪ Kodi n’zotheka kukhala ndi mtendere m’dziko la mavutoli? Onani masamba 10 mpaka 12.

▪ Kodi anthu apezadi chingalawa cha Nowa? Onani masamba 13 ndi 14.

▪ Kodi Abigayeli anali ndani, ndipo ifeyo tingaphunzirepo chiyani pa chikhulupiriro chake? Onani masamba 18 mpaka 21.

▪ Kodi Mulungu amavomereza mitala? Onani tsamba 30.