Tsamba 32
Tsamba 32
▪ Ngati muli wokhulupirika kwa Mulungu, kodi iye adzakudalitsani pokupatsani chuma? Onani tsamba 4.
▪ Kodi ndalama n’zimene zimapangitsa munthu kukhala wosangalaladi? Onani tsamba 9.
▪ Kodi pangakhale vuto ngati simukhulupirira kuti Adamu ndi Hava anali anthu enieni? Onani tsamba 12.
▪ Kodi mukuganiza kuti kubwezera n’kwabwino kapena n’koipa? Onani tsamba 20.
▪ Kodi mungapeze chiyani m’nyanja yaikulu ya ku Central America? Onani tsamba 25.