Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Kodi mzimu woyera ndi munthu? Onani tsamba 4 mpaka 7.

▪ Kodi Mulungu amafuna kuti tizichita zinthu zimene sitingathe? Onani tsamba 10.

▪ Kodi n’zotheka kuti munthu amene amakhulupirira kuti kulibe Mulungu ayambe kukhulupirira Mlengi? Onani tsamba 11 mpaka 14.

▪ Kodi Mdyerekezi ndi munthu weniweni? Onani tsamba 15.

▪ Kodi tikuphunzira chiyani kwa mtumwi Petulo amene anali ndi mtima wokayikakayika ndiponso mantha? Onani tsamba 21 mpaka 25.