Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

▪ Dziwani njira yabwino kwambiri yothetsera mavuto onse amene tikukumana nawo masiku ano. Onani tsamba 5.

▪ Anthu amene anapulumuka pamene mwana wasukulu anapha anthu pasukulu ina ku Winnenden, m’dziko la Germany, akufotokoza chimene chikuwathandiza kupirira zoopsazi. Onani tsamba 9.

▪ Kodi ndi Mfumu Herode uti amene ankafuna kupha Yesu ali wakhanda? Onani tsamba 13.

▪ Kodi mukudziwapo chiyani pachikondwerero chimene chimachitika ku Asia pakapita mwezi umodzi m’chaka chatsopano? Onani tsamba 20.

▪ Dziwani nkhani yokhudza nyimbo za m’nthawi ya Baibulo, pophunzira moyo wa Mfumu Davide. Onani tsamba 26.

▪ Panthawi imene Yesu anali modyeramo ziweto, kodi panabweradi mafumu atatu, kapena kuti anzeru a kum’mawa, kudzalambira? Onani tsamba 31.

[Mawu a Chithunzi patsamba 32]

Starving children: WHO/​OXFAM