Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi mungachite chiyani kuti musamamwe mowa mwauchidakwa? ONANI MASAMBA 6 MPAKA 9.

N’chifukwa chiyani muyenera kukhulupirira zimene Mulungu amalonjeza? ONANI TSAMBA 12.

N’chifukwa chiyani Mulungu anauza Aisiraeli kuti awononge Akanani? ONANI MASAMBA 13 MPAKA 15.

Kodi Akhristu oyambirira ankakhala m’nyumba zotani? ONANI MASAMBA 16 MPAKA 18.

Kodi anthu akufa amakhala ndi moyo kwinakwake? ONANI MASAMBA 19 MPAKA 21.