Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Dziwani chifukwa chake anthu masiku ano saopanso kuchimwa. ONANI TSAMBA 3 MPAKA 10.

Kodi n’chiyani chingatithandize kuti tizichita zinthu moona mtima ngakhale kuti anthu ambiri m’dzikoli ndi osaona mtima? ONANI TSAMBA 11 MPAKA 14.

Kodi nyenyezi zingakuthandizeni pa moyo wanu? ONANI TSAMBA 18 MPAKA 21.

Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani yoti anthu azipembedzo zosiyanasiyana azichitira pamodzi mapemphero? ONANI TSAMBA 27.

[Mawu a Chithunzi patsamba 32]

Stars: NASA, ESA, and A. Nota (STScI); Interfaith: REUTERS/​Andreas Manolis