Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi dziko lapansili lidzawonongedwa? ONANI TSAMBA 5.

Malinga ndi zimene Babulo limanena, kodi Mulungu adzathetsa chiyani? ONANI MASAMBA 5-6.

Mukakhumudwa ndi zimene mkazi kapena mwamuna wanu wachita, kodi n’chiyani chingakuthandizeni kuti mumulankhule mwaulemu? ONANI TSAMBA 12.

Kodi Yesu ananena kuti n’chiyani chingapangitse munthu kukhala wosangalala? ONANI TSAMBA 16.

Kodi n’kutheka kuti ntchito ya Yesu monga mmisiri wa matabwa inakhudza bwanji zimene ankaphunzitsa? ONANI MASAMBA 25-26.

[Mawu a Chithunzi patsamba 32]

U.S. National Archives photo