Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi Baibulo limati chiyani pa nkhani ya kutha kwa zoipa zonse? ONANI TSAMBA 5.

Kodi n’zotheka kuti nanunso mungasocheretsedwe ndi zimene mumakhulupirira? ONANI TSAMBA 10.

Kodi ziphunzitso za Calvin zimene anthu akhala akuzitsatira kwa zaka 500 tsopano zathandizadi? ONANI TSAMBA 18.

Kodi n’zoyenera kuti munthu akachimwa aziulula machimo ake? ONANI TSAMBA 22.

Kodi mkazi amene Kaini, mwana wa Adamu ndi Hava, anakwatira anachokera kuti? ONANI TSAMBA 25.

[Mawu a Chithunzi patsamba 32]

Engravings by Doré