Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi n’chifukwa chiyani anthu okha ndi amene amapemphera? ONANI TSAMBA 3.

Kodi Mulungu amayankhadi mapemphero athu? ONANI TSAMBA 11.

Kodi pali kusiyana kotani pa zimene Yesu ankachita pochiritsa anthu mozizwitsa ndi machiritso amene anthu amachita masiku ano? ONANI TSAMBA 13.

Kodi Baibulo lingatithandize bwanji kuti tisamangokhala ankhawa komanso achisoni? ONANI TSAMBA 19.

Kodi mzimu woyera ndi munthu? ONANI TSAMBA 26.