Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi n’zotheka kulankhula ndi amene amakhala kumwamba? ONANI TSAMBA 3-9.

Kodi ndi zoona kuti anthu otchulidwa m’Baibulo ankakhaladi ndi moyo zaka zambirimbiri? ONANI TSAMBA 12.

Kodi mayi wina anamva bwanji atagwira ntchito yothandiza anthu amene anavutika ndi chivomezi ku Haiti? ONANI TSAMBA 15.

Kodi inuyo mukanakhala kuti munalipo m’nthawi ya Yesu, mukanavomereza kuti iye ndi Mesiya? ONANI TSAMBA 18.

Kodi mungatani kuti muthandize makolo omwe sali pa banja? ONANI TSAMBA 22.