Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi ntchito yolalikira imene a Mboni za Yehova akugwira ikukwaniritsa ulosi wa m’Baibulo?

ONANI TSAMBA 9.

Kodi padziko lapansili zinthu zidzakhala bwanji Ufumu wa Mulungu ukamadzalamulira anthu onse?

ONANI TSAMBA 10.

Kodi makolo amene angobereka kumene, angatani ngati sakugwirizana pa nkhani ya mmene angalerere mwana wawoyo?

ONANI TSAMBA 11.

Kodi zoipa zinayamba bwanji?

ONANI TSAMBA 16.

N’chifukwa chiyani boma la Russia laletsa mabuku ena amene amafalitsidwa ndi Mboni za Yehova?

ONANI TSAMBA 18 MPAKA 21.