Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi Mulungu analengeranji dziko lapansili?

ONANI TSAMBA 4 MPAKA 6.

Kodi n’zotheka kukhala ndi moyo waphindu? Ngati n’zotheka, kodi mungatani kuti mukhale ndi moyo woterewo?

ONANI TSAMBA 7 MPAKA 9.

Kodi Ufumu umene Yesu anatiphunzitsa kuti tiziupempherera kuti ubwere, n’chiyani?

ONANI TSAMBA 16 MPAKA 17.

Kodi pali mtundu wa anthu womwe ndi wopambana kuposa mitundu ina?

ONANI TSAMBA 23.