Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi kutumizirana zithunzi ndiponso mauthenga okhudza kugonana pa foni za m’manja kapena pa Intaneti n’kulakwa?

ONANI TSAMBA 7.

Kodi Akhristu ayenera kumaona bwanji zinthu?

ONANI TSAMBA 13 NDI 14.

Kodi malamulo a Mulungu amatithandiza bwanji kukhala ndi thanzi labwino?

ONANI TSAMBA 16.

Kodi bambo angathandize bwanji mwana wake wamwamuna kuti azidzidalira?

ONANI TSAMBA 20.

Kodi n’koyenera kuti makolo aziphunzitsa ana awo nkhani zokhudza kugonana?

ONANI TSAMBA 29.