Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi n’chiyani chingatithandize kupirira masoka achilengedwe?

ONANI TSAMBA 6 NDI 7.

Kodi masoka achilengedwe adzatha?

ONANI TSAMBA 8 NDI 9.

Kodi pali aliyense amene angamasuliredi maulosi a m’Baibulo?

ONANI TSAMBA 11 MPAKA 13.

Kodi mukufuna kudziwa zimene mungachite kuti mupeze anzanu enieni?

ONANI TSAMBA 16 NDI 17.

Kodi Baibulo limatanthauza chiyani likamanena kuti pali “nthawi ya chikondi ndi nthawi ya chidani”?

ONANI TSAMBA 23 MPAKA 25.