Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi n’kuti kumene tingapeze mfundo zodalirika zokhudza Yesu?

ONANI TSAMBA 3 MPAKA 7.

Kodi Yehova amaderabe nkhawa anthu amene anasiya kumutumikira?

ONANI TSAMBA 10 NDI 11.

Kodi mnyamata wina anapeza bwanji bambo wachikondi amene ankalakalaka kuyambira ali mwana?

ONANI TSAMBA 14 NDI 15.

Kodi tingaphunzire chiyani kwa Yosefe, bambo wa Yesu?

ONANI TSAMBA 23 MPAKA 28.