Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Tsamba 32

Ngati Mulungu amamva mapemphero athu, n’chifukwa chiyani amalola kuti tizivutika?

ONANI TSAMBA 6 MPAKA 8.

Kodi n’chiyani chinathandiza mayi wina wa ku Philippines kuti asiye kumwa mowa mwauchidakwa komanso kuti banja lake liyambe kuyenda bwino?

ONANI TSAMBA 12 NDI 13.

Kodi Yehova akakhululukira munthu, ndiye kuti sakumbukiranso zolakwazo?

ONANI TSAMBA 18.

Kodi tingaphunzire chiyani pa chikondi komanso kukhulupirika kwa Rute?

ONANI TSAMBA 23 MPAKA 28.