Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo
ANA AZAKA ZOSAPITIRIRA ZITATU
Kalebe wamva zoti mnzake akudwala.
Iye akuti: “Ndadziwa chochita.
Ndimulembera kalata kuti ndimulimbikitse,
ndipo kenako ndikam’patsa.”Muzisonyeza ena chifundo ndipo nonse mudzakhala osangalala. 1 Petulo 3:8
ZOTI MAKOLO ACHITE
Muuzeni mwana wanuyo kuti aloze:
Nyumba
Tebulo
Kalebe
Dzuwa
Mbalame
Mtengo
Tchulani munthu amene akudwala ndipo kambiranani ndi mwanayo mmene mungamulimbikitsire.