Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsamba 32

Tsamba 32

Kodi mukuganiza kuti anthu ayenera kumachita chiyani pa nthawi ya Khirisimasi? Ndipo kodi pali zina zosangalatsa zimene anthu angamachite zoposa kukondwerera Khirisimasi?

ONANI TSAMBA 3 MPAKA 9.

Kodi mukudziwa chifukwa chake Mulungu anatumiza Yesu padziko lapansi?

ONANI TSAMBA 16 NDI 17.

Kodi mumakhulupirira kuti musanabadwe munakhalapo ndi moyo kwinakwake? Anthu ena amakhulupirira choncho, koma kodi n’chifukwa chiyani iwo amakhulupirira zimenezi?

ONANI TSAMBA 18 MPAKA 20.

Kodi kale akazi ankagwiritsa ntchito chiyani podzikongoletsa?

ONANI TSAMBA 24 MPAKA 26.