Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Rabeka

Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo—Rabeka

Mumavidiyo akuti Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo, muli zitsanzo za anthu osiyanasiyana otchulidwa m’Baibulo omwe anasonyeza kuti anali ndi chikhulupiriro cholimba. Muvidiyoyi tiona zomwe tingaphunzire kuchokera kwa Rabeka komanso chifukwa chake tiyenera kumutsanzira.