Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zifukwa Zokhalira ndi Chikhulupiriro—Kodi Ndiziyendera Mfundo za Mulungu Kapena Zanga?

Zifukwa Zokhalira ndi Chikhulupiriro—Kodi Ndiziyendera Mfundo za Mulungu Kapena Zanga?

Hugo ndi Clara akufotokoza mmene kutsatira mfundo za Yehova pa nthawi imene anali kusukulu kunawathandizira kuti asamatengere zochita za anzawo komanso kupewa mavuto amene anzawowo anakumana nawo.