Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Zifukwa Zokhalira ndi Chikhulupiriro—Kodi Zinangokhalapo Zokha Kapena Zinachita Kulengedwa?

Zifukwa Zokhalira ndi Chikhulupiriro—Kodi Zinangokhalapo Zokha Kapena Zinachita Kulengedwa?

Pali zinthu zambiri zomwe zingachititse munthu kukayikira zomwe amakhulupirira. Achinyamata akufotokoza zifukwa zomwe zimawachititsa kukhulupirira kuti zinthu zinachita kulengedwa.