Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba

Danieli ali kutali ndi kwawo ndipo chikhulupiriro chake chikuyesedwa pamene akuyesetsa kuyembekezera Yehova.

Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba​—Mbali Yoyamba

Danieli ali kutali ndi makolo ake komanso mzinda wakwawo wawonongedwa, kodi iye akhalabe pa ubwenzi ndi Mulungu wake Yehova?

Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba​—Mbali Yachiwiri

Ufumu wina wamphamvu wayamba kulamulira. Danieli wakumana ndi adani ena atsopano. Chikhulupiriro chake chikuyesedwa kwambiri kuposa kale.