Danieli Anali Munthu Wachikhulupiriro Cholimba—Mbali Yachiwiri
Ufumu wina wamphamvu wagonjetsa Babulo n’kuyamba kulamulira ndipo Danieli wakumana ndi adani ena atsopano. Chikhulupiriro chake chikuyesedwa kwambiri kuposa poyamba.