Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Mafumu

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 1 Mafumu

Mulungu anadalitsa kwambiri Solomo. Koma pang’ono ndi pang’ono, iye anayamba kupanduka n’kumalambira milungu yonyenga, ndipo izi zinachititsa kuti ufumu wa Isiraeli ugawikane.