Phunziro 10 Kusinthasintha Mawu YAMBANI Kusinthasintha Mawu Kodi kusintha mphamvu ya mawu athu, kamvekedwe komanso liwiro kumathandiza bwanji omvetsera athu? Pepani, zalephereka. Koperani Vidiyoyi Yam'mbuyo Yotsatira Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kuwerenga ndi Kuphunzitsa—Kusinthasintha Mawu Pena muzilankhula mofulumira, pena mwapang’onopang’ono, pena mokweza, pena motsitsa komanso pena muzilankhula ndi mawu aakulu, pena aang’ono. Muzichita zimenezi n’cholinga choti muzifika anthu pamtima n’kuwathandiza kuti azitsatira zimene akuphunzira. Sindikizani Patsani ena Patsani ena Kusinthasintha Mawu MAVIDIYO A KUWERENGA KOMANSO KUPHUNZITSA MWALUSO Kusinthasintha Mawu Chichewa Kusinthasintha Mawu https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102019369/univ/art/1102019369_univ_sqr_xl.jpg