Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”

Nehemiya akutsogolera pa ntchito yomanganso mpanda wa Yerusalemu komanso kubwezeretsa kulambira koona.

Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”​—Mbali Yoyamba

Nehemiya akupitirizabe kumanga mpanda ngakhale kuti pali otsutsa ambiri.

Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”—Mbali Yachiwiri

Mpanda wamalizidwa, koma kodi Nehemiya achita chiyani kuti alimbitse chikhulupiriro cha anthuwo?