Nehemiya: “Chimwemwe Chimene Yehova Amapereka Ndicho Malo Anu Achitetezo”—Mbali Yoyamba
Nehemiya wasiya ntchito yake kunyumba yachifumu ku Susani n’cholinga choti akamangenso mpanda wa mzinda waukulu wa Yehova. Koma akukumananso ndi mayesero ena kuwonjezera pa ntchito yaikulu yomanganso mpanda. Kodi pemphero komanso kulimba mtima, zimuthandiza bwanji kuti amalize ntchitoyo?