Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 77

Kuwala M’dziko Lamdima

Kuwala M’dziko Lamdima

(2 Akorinto 4:6)

  1. 1. M’dzikoli mulitu mdima.

    Anthu sakumvera.

    Kuwala kwatifikira

    Ngati m’bandakucha.

    (KOLASI)

    Uthenga wa M’lungu

    Wawala ngati dzuwa

    M’dziko lamdimali.

    Ukupatsa anthu

    Onse chiyembekezo.

    Mdima watha.

  2. 2. Tidzutse omwe agona

    Poti nthawi yatha.

    Komanso tiwathandize

    Tiwapempherere.

    (KOLASI)

    Uthenga wa M’lungu

    Wawala ngati dzuwa

    M’dziko lamdimali.

    Ukupatsa anthu

    Onse chiyembekezo.

    Mdima watha.