Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Ima Uone

Ima Uone

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Kuotherako moto, Kuona nyenyezi

    Ka mphepo kabwino kakuwombanso, macheza akukoma.

    Kuiwala mavuto, kuona zabwino

    Uzipezako nthawi yoganizira ntchito za M’lunguzi.

    (KOLASI)

    Ima kaye uoneko chilengedwe.

    Phunzira makhalidwe a M’lungu.

    Uzipezako nthawi yoganizira.

    Pang’ono chabe,

    Ima, uone.

  2. 2. Yang’ana m’mwamba uone kuwala kwa mweziwu

    Zinthu zakumwamba zikulengeza ulemerero wa M’lungu.

    Kaya mavuto akule, tione mtsogolo.

    Tizipeza mphamvu tikadziwa kuti Yehova ali nafe.

    (KOLASI)

    Ima kaye uoneko chilengedwe.

    Phunzira makhalidwe a M’lungu.

    Uzipezako nthawi yoganizira.

    Pang’ono chabe,

    Ima, uone.

    Ima, uone.

    Ima, uone.

    (KOLASI)

    Ima kaye uoneko chilengedwe.

    Phunzira makhalidwe a M’lungu.

    Uzipezako nthawi yoganizira.

    Pang’ono chabe,

    Ima, uone.

    (KUMALIZA)

    Tisiye zonse tioneko

    Pang’ono chabe

    Usiye zonse uoneko.

    Ima pang’ono chabe

    Ima uone.