Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mphamvu Yoposa Yanga

Mphamvu Yoposa Yanga

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. M’lungu wanga, ndalemedwa

    Ndi mavuto ndi kuda nkhawa.

    Ndikudziwatu kuti inu

    M’lungu wanga,

    Mundithandiza.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Yehova

    Ndipatseni mzimu wanu.

    (KOLASI)

    Ndipeze mphamvu

    Ndikhaletu ngati ndikuuluka.

    Ngati Chiwombankhanga chomwe

    Chadzitambasula, ndipatseni

    Mphamvu yoposa yanga.

  2. 2. Mphamvu zomwe m’mandipatsa

    Ndimathandizira anthu ena.

    Amadziwa kuti inu

    M’lungu wawo, m’mawakonda.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Yehova

    Ndipatseni mzimu wanu.

    (KOLASI)

    Ndipeze mphamvu

    Ndikhaletu ngati ndikuuluka.

    Ngati Chiwombankhanga chomwe

    Chadzitambasula, ndipatseni

    Mphamvu yoposa yanga.

    (KOLASI)

    Ndipeze mphamvu

    Ndikhaletu ngati ndikuuluka.

    Ngati Chiwombankhanga chomwe

    Chadzitambasula, ndipatseni

    Mphamvu yoposa yanga.

    Mphamvu yoposa yanga.

    Mphamvu yoposa yanga.