Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mabwenzi Enieni

Mabwenzi Enieni

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Masikuwa moyo ukuvuta, patokha n’zovuta.

    Yehova amadziwa tikufunika mabwenzi

    Kodi mabwenzi enieni tingawapeze kuti?

    Paja Malemba amatiuza.

    (KOLASI)

    Bwenzi

    Lenilenidi

    Limakukonda,

    Pamtendere, pamavuto,

    Limalangiza,

    Kukuyamikira,

    Kukulimbikitsa zabwino,

    Kuti uzikonda kwambiri M’lungu.

    Bwenzi labwino.

  2. 2. Nthawi zonse limakonda. Malemba ’kutero.

    Pamavuto onse usagonjetu. Pemphera; zisiye.

    Tiyesetse kugwirizana ndi anthu amisinkhu yonse,

    Tonse tidzakhala m’Paradaiso.

    (KOLASI)

    Bwenzi

    Lenilenidi

    Limakukonda,

    Pamtendere, pamavuto,

    Limalangiza,

    Kukuyamikira,

    Kukulimbikitsa zabwino,

    Kuti uzikonda kwambiri M’lungu.

    Bwenzi labwino.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Lothandiza,

    Lokondanso kutumikira Yehova,

    Limalimbikitsa, kukutonthoza, n’kumvetsa.

    Bwenzi labwino.

    (KOLASI)

    Bwenzi

    Lenilenidi

    Limakukonda,

    Pamtendere, pamavuto,

    Limalangiza,

    Kukuyamikira,

    Kukulimbikitsa zabwino,

    Kuti uzikonda kwambiri M’lungu.

    Bwenzi labwino.

    (KOLASI)

    Bwenzi

    Lenilenidi

    Limakukonda,

    Pamtendere, pamavuto,

    Limalangiza,

    Kukuyamikira,

    Kukulimbikitsa zabwino,

    Kuti uzikonda kwambiri M’lungu.

    Bwenzi labwino.

    Bwenzilitu.

    O, n’lenileni.