Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

“Menya Nkhondo Yabwino Yosunga Chikhulupiriro”

“Menya Nkhondo Yabwino Yosunga Chikhulupiriro”

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Pena ndimangomva ngati

    Ndavutitsidwa mokwanira.

    Moti ndimakhumudwadi

    Ndimafuna nditangosiya.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Yehova andithandiza

    Moti ndizichita zoyenera

    N’zikonda cho’nadi.

    Ndimva Yehova akuti:

    (KOLASI)

    Inetu posachedwa,

    Ndikupukuta misozi.

    Posachedwatu pompa

    M’dziko latsopano

    Ukhulupirike.

    Ndithu upambana—

    (Na)

    Ndithu upambana.

  2. 2. Mawu ake andithandiza.

    M’mavuto iye anditeteza.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Yehova andithandiza

    Ndadziwa zochita n’kakhumudwa

    N’zikonda cho’nadi.

    Ndimva Yehova akuti:

    (KOLASI)

    Inetu posachedwa,

    Ndikupukuta misozi.

    Posachedwatu pompa

    M’dziko latsopano

    Ukhulupirike.

    Ndithu upambana—

    (Na)

    Ndithu upambana.

    Ndithu upambana.

    Ndithu upambana.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Ndithu upambana

    Ndikuthandiza,

    Upambanatu.

    (KOLASI)

    Inetu posachedwa,

    Ndikupukuta misozi.

    Posachedwatu pompa

    M’dziko latsopano.

    Ukhulupirike.

    Ndithu upambana.