Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mutulire Yehova

Mutulire Yehova

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Dzulotu n’taimba,

    N’nadziwa suli bwino.

    Komatu Yehova

    Amakukondadi.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Limba mtima.

    Ukagwa akudzutsa.

    (KOLASI)

    M’khulupirire; limbabe.

    Usaope; um’dalire.

    Suli wekha; pemphera.

    Amamvatu; akumvetsa.

    Muuze Yehova.

    Mutulire. Mutulire. Mutulire.

  2. 2. Yang’ana uone;

    Dzikotu likubwera

    Mavuto adzatha

    Chifukwatu cha dipo.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Dikirabe,

    Tipirirebetu ndithu

    Ndiye

    (KOLASI)

    M’khulupirire; limbabe.

    Usaope; um’dalire.

    Alipotu; tim’pemphe.

    Atimvatu; atimvetsa.

    Timu’ze Yehova.

    Tim’tulire. Tim’tulire. Tim’tulire.

    (KOLASI)

    M’khulupirire; limbabe.

    Usaope; um’dalire.

    Alipotu; tim’pemphe.

    Atimvatu; Atimvetsa.

    Timu’ze Yehova.

    Tim’tulire. Tim’tulire. Tim’tulire.

    Tim’tulire. Tim’tulire.