Musathamange
Pangani Dawunilodi:
1. Yendani m’sathamange.
Inde mukusangalala.
Koma pakakhala anthu,
Simuyeneratu,
Kuthamanga.
(KOLASI)
M’sathamange.
Ndi bwinotu mufatse.
Mudzapeza chimwemwe.
M’sathamange.
2. Inde muli n’zochita
Komanso anthu owathandiza
Komatu m’saiwale.
Muwasonyeze,
Mumawakonda.
(KOLASI)
M’sathamange.
Ndi bwinotu mufatse.
Mudzapeza chimwemwe.
M’sathamange.
3. Mungafulumire ndithu.
Pokagogoda
Khomo lamunthu
N’kufufuza eni khomo
Koma odutsa
Chezani nawo.
(KOLASI)
M’sathamange.
Ndi bwinotu mufatse.
Mudzapeza chimwemwe.
M’sathamange
O. M’sathamange.